Ndakatulo nchiyani ndafuna ndidziwe?

Ndimawu ophiphiritsa kodi?

Kapena zining'a zakuthwa ndinso mawu ozama?

Odziwano tafotokozani

Osamanu phunzitseni

B. W. Malunga, Ndakatulo nchiyani?